Skip to content Skip to sidebar Skip to footer

(Download) "Luso la Utumiki" by Dag Heward-Mills * eBook PDF Kindle ePub Free

Luso la Utumiki

📘 Read Now     📥 Download


eBook details

  • Title: Luso la Utumiki
  • Author : Dag Heward-Mills
  • Release Date : January 11, 2019
  • Genre: Christianity,Books,Religion & Spirituality,
  • Pages : * pages
  • Size : 731 KB

Description

Kukuza luso ndiko kukuza kuthekera. Baibulo limanena kuti kukonderedwa kumadza kwa anthu a luso. Ntchito ya utumiki imafuna kuthekera kwa kukulu.
Bukhu latsopanoli, “Luso la Utumiki” ndi lofunika kwambiri kwa onse amene amakhumbira kuchita ntchito ya Mulungu. Limawonetseratu maganizo omwe ali olondola ndi oipa okhudzana ndi utumiki, chomwe ntchito ya utumiki chiri, chomwe mukuyenera kuchita ngati wogwira ntchito mu utumiki ndi momwe mungapangire ntchito za mtumiki.
Mwadabwapo zokhuzana ndi momwe mungachitire ntchito ya utumiki? Bukhu lapaderali lolembedwa ndi Dag Heward-Mills likakulimbikitsani inu kuyenda moyenereza maitanidwe an a Mulungu ndi kukutsogozani inu mu kudzipereka nokha kwathunthu ku ntchito ya Mulungu.


Download Books "Luso la Utumiki" PDF ePub Kindle